Koma Yesu m'mene anadziwa, anachokera kumeneko: ndipo anamtsata Iye anthu ambiri; ndipo Iye anawachiritsa iwo onse,
Mateyu 19:2 - Buku Lopatulika Ndipo makamu aakulu a anthu anamtsata; ndipo Iye anawachiritsa kumeneko. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo makamu akulu a anthu anamtsata; ndipo Iye anawachiritsa kumeneko. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anthu ambirimbiri adamtsata, ndipo Iye ankachiritsa odwala kumeneko. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Magulu akulu a anthu anamutsatira Iye, ndipo iwo anachiritsidwa pomwepo. |
Koma Yesu m'mene anadziwa, anachokera kumeneko: ndipo anamtsata Iye anthu ambiri; ndipo Iye anawachiritsa iwo onse,
Ndipo Afarisi anadza kwa Iye, namuyesa, nanena, Kodi nkuloledwa kuti munthu achotse mkazi wake pa chifukwa chilichonse?