ndi kuti mungakweze maso anu kupenya kumwamba, ndipo poona dzuwa ndi mwezi ndi nyenyezi, khamu lonse la kumwamba, munganyengedwe ndi kuzigwadira, ndi kuzitumikira, zimene Yehova Mulungu wanu anagawira mitundu yonse ya anthu pansi pa thambo lonse.
Masalimo 19:3 - Buku Lopatulika Palibe chilankhulidwe, palibe mau; liu lao silimveka. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Palibe chilankhulidwe, palibe mau; liu lao silimveka. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Palibe kulankhula, palibe kunena mau aliwonse. Liwu lao silimveka konse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Palibe kuyankhula, palibe mawu aliwonse; liwu lawo silimveka. |