Ndipo mbiri yake inabuka ku Siriya konse: ndipo anatengera kwa Iye onse akudwala, ogwidwa ndi nthenda ndi mazunzo a mitundumitundu, ndi ogwidwa ndi ziwanda, ndi akhunyu, ndi amanjenje; ndipo Iye anawachiritsa.
Marko 2:3 - Buku Lopatulika Ndipo anadza kwa Iye otenga munthu wodwala manjenje, wonyamulidwa ndi anthu anai. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anadza kwa Iye otenga munthu wodwala manjenje, wonyamulidwa ndi anthu anai. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anthu ena anai adaanyamula munthu wa ziwalo zakufa, kubwera naye kwa Yesu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Amuna anayi anabwera, atanyamula munthu wofa ziwalo. |