ndipo anati, nanena naye, Mutiuze muchita izi ndi ulamuliro wotani? Kapena ndani iye amene anakupatsani ulamuliro umene?
Luka 20:3 - Buku Lopatulika Ndipo anayankha, nati kwa iwo, Ndidzakufunsani mau Inenso; mundiuze: Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anayankha, nati kwa iwo, Ndidzakufunsani mau Inenso; mundiuze: Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yesu adati, “Nanenso ntakufunsani funso limodzi. Tandiwuzani, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iye anayankha kuti, “Inenso ndikufunsani, mundiyankhe, |
ndipo anati, nanena naye, Mutiuze muchita izi ndi ulamuliro wotani? Kapena ndani iye amene anakupatsani ulamuliro umene?
Mau anu akhale m'chisomo, okoleretsa, kuti mukadziwe inu mayankhidwe anu a kwa yense akatani.