ndiika utawaleza wanga m'mtambomo, ndipo udzakhala chizindikiro cha pangano lopangana ndi Ine ndi dziko lapansi.
Genesis 9:14 - Buku Lopatulika Ndipo padzakhala pophimba ndi mtambo Ine dziko lapansi, utawo udzaoneka m'mtambomo; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo padzakhala pophimba ndi mtambo Ine dziko lapansi, utawo udzaoneka m'mtambomo; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Nthaŵi zonse pakakhala mitambo mu mlengalenga, ndipo pakaoneka utawaleza m'mitambomo, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Nthawi zonse pakakhala mitambo mu mlengalenga ndipo utawaleza uwoneka, |
ndiika utawaleza wanga m'mtambomo, ndipo udzakhala chizindikiro cha pangano lopangana ndi Ine ndi dziko lapansi.
ndipo ndidzakumbukira pangano langa limene lili ndi Ine ndi inu, ndi zamoyo zonse zokhala ndi moyo; ndipo madzi sadzakhalanso konse chigumula chakuononga zamoyo zonse.
Amene aphimba thambo ndi mitambo, amene akonzera mvula nthaka, amene aphukitsa msipu pamapiri.