ndipo anakhala ndi moyo Enosi, atabala Kenani, zaka mazana asanu ndi atatu kudza khumi ndi zisanu: ndipo anabala ana aamuna ndi aakazi.
Genesis 5:9 - Buku Lopatulika Ndipo Enosi anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi anai, nabala Kenani; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Enosi anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi anai, nabala Kenani; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Enosi ali wa zaka 90, adabereka mwana dzina lake Kenani, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamene Enosi anali ndi zaka 90, anabereka Kenani. |
ndipo anakhala ndi moyo Enosi, atabala Kenani, zaka mazana asanu ndi atatu kudza khumi ndi zisanu: ndipo anabala ana aamuna ndi aakazi.
masiku ake onse a Seti anali zaka mazana asanu ndi anai kudza khumi ndi ziwiri; ndipo anamwalira.
mwana wa Metusela, mwana wa Enoki, mwana wa Yaredi, mwana wa Mahalalele, mwana wa Kainani,