ndipo Kenani anakhala ndi moyo, atabala Mahalalele zaka mazana asanu ndi atatu kudza makumi anai, ndipo anabala ana aamuna ndi aakazi;
Genesis 5:14 - Buku Lopatulika masiku ake onse a Kenani anali zaka mazana asanu ndi anai kudza khumi; ndipo anamwalira. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 masiku ake onse a Kenani anali zaka mazana asanu ndi anai kudza khumi; ndipo anamwalira. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adamwalira ali wa zaka 910. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zaka zonse za Kenani zinali 910, ndipo anamwalira. |
ndipo Kenani anakhala ndi moyo, atabala Mahalalele zaka mazana asanu ndi atatu kudza makumi anai, ndipo anabala ana aamuna ndi aakazi;
Ndipo Mahalalele anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi limodzi kudza zisanu, nabala Yaredi;
Masiku ake onse anakhala ndi moyo Adamu anali zaka mazana asanu ndi anai, kudza makumi atatu; ndipo anamwalira.