ndipo anakhala ndi moyo Enosi, atabala Kenani, zaka mazana asanu ndi atatu kudza khumi ndi zisanu: ndipo anabala ana aamuna ndi aakazi.
Genesis 5:11 - Buku Lopatulika Masiku ake onse a Enosi anali mazana asanu ndi anai kudza zisanu; ndipo anamwalira. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Masiku ake onse a Enosi anali mazana asanu ndi anai kudza zisanu; ndipo anamwalira. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adamwalira ali wa zaka 905. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zaka zonse za Enosi pamodzi zinali 905 ndipo anamwalira. |
ndipo anakhala ndi moyo Enosi, atabala Kenani, zaka mazana asanu ndi atatu kudza khumi ndi zisanu: ndipo anabala ana aamuna ndi aakazi.
Masiku ake onse anakhala ndi moyo Adamu anali zaka mazana asanu ndi anai, kudza makumi atatu; ndipo anamwalira.