Koma maso a Israele anali akhungu mu ukalamba wake, ndipo sanathei kuona. Ndipo anadza nao pafupi; ndipo anapsompsona iwo, nawafungatira.
Genesis 48:8 - Buku Lopatulika Ndipo Israele anayang'ana ana aamuna a Yosefe, nati, Ndani awa? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Israele anayang'ana ana amuna a Yosefe, nati, Ndani awa? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yakobe ataona ana a Yosefe, adafunsa kuti, “Nanga anyamata aŵa nga yani?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Israeli ataona ana a Yosefe anafunsa kuti, “Anyamatawa ndi a yani?” |
Koma maso a Israele anali akhungu mu ukalamba wake, ndipo sanathei kuona. Ndipo anadza nao pafupi; ndipo anapsompsona iwo, nawafungatira.
Ndipo Yosefe anati kwa atate wake, Amenewa ndi ana anga, amene Mulungu wandipatsa ine pano. Ndipo iye anati, Udze naotu kwa ine, ndipo ndidzawadalitsa.
Funani Yehova, ndipo mudzakhala ndi moyo; angabuke ngati moto m'nyumba ya Yosefe, ndipo unganyeke wopanda wakuzima mu Betele;