Ndipo pamene zinadya sizinadziwike kuti zinadya; koma zinaipabe m'maonekedwe ao monga poyamba.
Genesis 41:22 - Buku Lopatulika Pamenepo ndinauka. Ndipo ndinaona m'kulota kwanga, taona, ngala zisanu ndi ziwiri zinamera pa mbuwa imodzi zodzala ndi zabwino; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pamenepo ndinauka. Ndipo ndinaona m'kulota kwanga, taona, ngala zisanu ndi ziwiri zinamera pa mbuwa imodzi zodzala ndi zabwino; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Nditagonanso ndidalota ntaona ngala zatirigu zisanu ndi ziŵiri zakucha ndi zokhwima bwino zitabala pa mphesi imodzi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Nditagonanso kachiwiri, ndinalota ngala zisanu ndi ziwiri za tirigu zathanzi ndi zonenepa zitabala pa phata limodzi. |
Ndipo pamene zinadya sizinadziwike kuti zinadya; koma zinaipabe m'maonekedwe ao monga poyamba.
ndipo, taona, ngala zisanu ndi ziwiri zina zofota, zoonda, zopserera ndi mphepo ya kum'mawa, zinamera pambuyo pao;