Ndipo anati, Yehova, Mulungu wa mbuyanga Abrahamu mundiyendetse ine bwino lero lino, mumchitire ufulu mbuyanga Abrahamu.
Genesis 27:10 - Buku Lopatulika ndipo udzapita nacho kwa atate wako, kuti adye, ndi kukudalitsa iwe asanafe. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndipo udzapita nacho kwa atate wako, kuti adye, ndi kukudalitsa iwe asanafe. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ukapereke chakudyacho kwa bambo wako kuti akadye, ndipo akudalitse asanafe.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka upite nacho chakudyacho kwa abambo ako kuti adye ndi kukudalitsa asanafe.” |
Ndipo anati, Yehova, Mulungu wa mbuyanga Abrahamu mundiyendetse ine bwino lero lino, mumchitire ufulu mbuyanga Abrahamu.
Yakobo ndipo anati kwa Rebeka amake, Taonani, Esau mkulu wanga ndiye munthu waubweya, ine ndine munthu wosalala.
Pitatu kubusa, ukanditengere ine kumeneko tiana tiwiri tabwino tambuzi; ndikonzere nato chakudya chokolera cha atate wako chonga chomwe achikonda: