Ndipo Isaki anachoka kumeneko, namanga hema wake m'chigwa cha Gerari, nakhala kumeneko.
Genesis 26:16 - Buku Lopatulika Ndipo Abimeleki anati kwa Isaki, Uchoke kwa ife chifukwa kuti iwe uli wamphamvu wopambana ife. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Abimeleki anati kwa Isaki, Uchoke kwa ife chifukwa kuti iwe uli wamphamvu wopambana ife. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono Abimeleki adauza Isaki kuti, “Muchoke kuno. Inu ndinu amphamvu kupambana ife.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo Abimeleki anati kwa Isake, “Muchoke pakati pathu chifukwa mwasanduka wamphamvu kuposa ife.” |
Ndipo Isaki anachoka kumeneko, namanga hema wake m'chigwa cha Gerari, nakhala kumeneko.
Ndipo ananena ndi anthu ake, Taonani, anthu, ndiwo ana a Israele, achuluka, natiposa mphamvu.