Ndipo Abrahamu anati kwa mnyamata wake wamkulu wa pa nyumba yake, amene analamulira pa zonse anali nazo, Taikatu dzanja lako pansi pa ntchafu yanga:
Genesis 24:34 - Buku Lopatulika Ndipo anati, Ine ndine mnyamata wa Abrahamu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anati, Ine ndine mnyamata wa Abrahamu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Iyeyo adati, “Ine ndine wantchito wa Abrahamu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Motero iye anati, “Ine ndine wantchito wa Abrahamu. |
Ndipo Abrahamu anati kwa mnyamata wake wamkulu wa pa nyumba yake, amene analamulira pa zonse anali nazo, Taikatu dzanja lako pansi pa ntchafu yanga:
Ndipo anaika chakudya pamaso pake: koma anati, Sindidzadya ndisananene chimene ndadzera. Ndipo anati, Nenatu.