Koma mthenga wa Yehova anamuitana iye ndi mau odzera kumwamba, nati, Abrahamu, Abrahamu; ndi iye anati, Ndine pano.
Genesis 22:10 - Buku Lopatulika Ndipo Abrahamu anatambasula dzanja lake, natenga mpeni kuti amuphe mwana wake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Abrahamu anatambasula dzanja lake, natenga mpeni kuti amuphe mwana wake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono adasolola mpeni kuti amuphe mwana wakeyo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka Abrahamu anatambasula dzanja lake natenga mpeni kuti aphe mwana wake. |
Koma mthenga wa Yehova anamuitana iye ndi mau odzera kumwamba, nati, Abrahamu, Abrahamu; ndi iye anati, Ndine pano.
Ndipo anafika kumalo komwe Mulungu anamuuza iye; ndipo Abrahamu anamanga guwa la nsembe nakonza nkhuni, namanga Isaki mwana wake, namuika iye paguwa la nsembe pamwamba pa nkhuni.