Genesis 11:23 - Buku Lopatulika ndipo Serugi anakhala ndi moyo zaka mazana awiri, atabala Nahori, nabala ana aamuna ndi aakazi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndipo Serugi anakhala ndi moyo zaka mazana awiri, atabala Nahori, nabala ana aamuna ndi aakazi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pambuyo pake adakhala ndi moyo zaka zina 200, ndipo adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atabereka Nahori, Serugi anakhala ndi moyo zaka zina 200 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi. |