Genesis 11:17 - Buku Lopatulika ndipo Eberi anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza makumi awiri, atabala Pelegi, nabala ana aamuna ndi aakazi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndipo Eberi anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza makumi awiri, atabala Pelegi, nabala ana aamuna ndi aakazi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pambuyo pake adakhala ndi moyo zaka zina 430, ndipo adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atabereka Pelegi, Eberi anakhala ndi moyo zaka zina 430 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi. |