Genesis 11:12 - Buku Lopatulika Ndipo Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza zisanu nabala Sela; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza zisanu nabala Sela; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene Aripakisadi anali wa zaka 35, adabereka mwana dzina lake Sela. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamene Aripakisadi anali ndi zaka 35, anabereka Sela. |
ndipo Semu anakhala ndi moyo zaka mazana asanu, atabala Aripakisadi, nabala ana aamuna ndi aakazi.
ndipo Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza zitatu, atabala Sela, nabala ana aamuna ndi aakazi.