1 Mbiri 1:18 - Buku Lopatulika18 Ndi Aripakisadi anabala Sela; ndi Sela anabala Eberi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndi Aripakisadi anabala Sela; ndi Sela anabala Eberi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Aripakisadi adabereka Sela. Sela adabereka Ebere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Aripakisadi anabereka Sela ndipo Selayo anabereka Eberi: Onani mutuwo |