Genesis 10:30 - Buku Lopatulika Kwao kunayamba pa Mesa pakunka ku Sefari phiri la kum'mawa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Kwao kunayamba pa Mesa pakunka ku Sefari phiri la kum'mawa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Dziko limene ankakhalamo lidayambira ku Mesa kumaloŵa ku Sefari ku mapiri chakuvuma. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Chigawo chimene ankakhala chinayambira ku Mesa mpaka ku Seferi, ku dera la mapiri chakummawa. |
Amenewa ndi ana a Semu, monga mwa mabanja ao, mwa zinenedwe zao, m'maiko ao, m'mitundu yao.
Ndipo ananena fanizo lake, nati, Ku Aramu ananditenga Balaki, mfumu ya Mowabu ananditenga ku mapiri a kum'mawa, Idza, udzanditembererere Yakobo. Idza, nudzanyoze Israele.