Genesis 10:3 - Buku Lopatulika Ndi ana aamuna a Gomeri: Asikenazi, ndi Rifati, ndi Togarima. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi ana amuna a Gomeri: Asikenazi, ndi Rifati, ndi Togarima. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ana a Gomeri anali Asikenazi, Rifati ndi Togarima. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ana aamuna a Gomeri anali: Asikenazi, Rifati ndi Togarima. |
Kwezani mbendera m'dziko, ombani lipenga mwa amitundu, konzerani amitundu amenyane naye, mummemezere maufumu a Ararati, Mini, ndi Asikenazi; muike nduna; amenyane naye; mukweretse akavalo ngati dzombe.
Iwo a nyumba ya Togarima anagula malonda ako ndi akavalo, ndi akavalo a nkhondo, ndi nyuru.
Gomeri ndi magulu ake onse, nyumba ya Togarima, ku malekezero a kumpoto, ndi magulu ake onse, mitundu yambiri pamodzi ndi iwe.