Ana a Semu: Elamu, ndi Asiriya, ndi Aripakisadi, ndi Ludi, ndi Aramu, ndi Uzi, ndi Huli, ndi Getere, ndi Meseki.
Genesis 10:23 - Buku Lopatulika Ndi ana a Aramu: Uzi ndi Huli ndi Getere, ndi Masi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi ana a Aramu: Uzi ndi Huli ndi Getere, ndi Masi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ana a Aramu anali Uzi, Hulu, Getere ndi Masi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ana aamuna a Aramu anali: Uzi, Huri, Geteri ndi Mesaki. |
Ana a Semu: Elamu, ndi Asiriya, ndi Aripakisadi, ndi Ludi, ndi Aramu, ndi Uzi, ndi Huli, ndi Getere, ndi Meseki.
Panali munthu m'dziko la Uzi, dzina lake ndiye Yobu; ndipo munthuyu anali wangwiro ndi woongoka, wakuopa Mulungu ndi kupewa zoipa.
ndi anthu onse osakanizidwa, ndi mafumu onse a dziko la Uzi, ndi mafumu onse a dziko la Afilisti, ndi Asikeloni, ndi Gaza, ndi Ekeroni, ndi otsala a Asidodi,