M'dziko momwemo iye anatuluka kunka ku Asiriya, namanga Ninive, ndi mzinda wa Rehoboti, ndi Kala,
Genesis 10:12 - Buku Lopatulika ndi Reseni pakati pa Ninive ndi Kala: umenewo ndi mzinda waukulu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi Reseni pakati pa Ninive ndi Kala: umenewo ndi mudzi waukulu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ndi mzinda wa Reseni umene uli pakati pa Ninive ndi mzinda waukulu uja wa Kala. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ndi Reseni, mzinda waukulu umene uli pakati pa Ninive ndi Kala. |
M'dziko momwemo iye anatuluka kunka ku Asiriya, namanga Ninive, ndi mzinda wa Rehoboti, ndi Kala,
Meseki, Tubala, ndi aunyinji ake onse ali komweko, manda ake amzinga; onsewo osadulidwa, ophedwa ndi lupanga; pakuti anaopsetsa m'dziko la amoyo.