Ndipo Mose anali nazo zaka makumi asanu ndi atatu, ndi Aroni anali nazo zaka makumi asanu ndi atatu kudza zitatu, pamene ananena ndi Farao.
Eksodo 7:8 - Buku Lopatulika Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, ndi kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, ndi kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono Chauta adauza Mose ndi Aroni kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yehova anati kwa Mose ndi Aaroni, |
Ndipo Mose anali nazo zaka makumi asanu ndi atatu, ndi Aroni anali nazo zaka makumi asanu ndi atatu kudza zitatu, pamene ananena ndi Farao.
Pamene Farao adzalankhula nanu, ndi kuti, Dzichitireni chodabwitsa; pamenepo uzinena ndi Aroni, Tenga ndodo yako, iponye pansi pamaso pa Farao, isanduke chinjoka.
ndi zizindikiro zake, ndi ntchito zake, adazichitira Farao mfumu ya Aejipito, ndi dziko lake lonse pakati pa Ejipito;