Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 7:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Yehova anati kwa Mose ndi Aaroni,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

8 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Tsono Chauta adauza Mose ndi Aroni kuti,

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 7:8
3 Mawu Ofanana  

Mose anali ndi zaka 80, ndipo Aaroni anali ndi zaka 83 pamene anakayankhula kwa Farao.


“Ngati Farao adzati kwa inu, ‘Chitani chozizwitsa,’ iwe Mose udzati kwa Aaroni, ‘Tenga ndodo yako ndipo uyiponye pamaso pa Farao,’ ndipo idzasanduka njoka.”


zizindikiro zozizwitsa zimene anazionetsa ndi zinthu zimene anazichita mʼkati mwa Igupto, Farao mfumu ya Igupto ndi kwa dziko lake lonse;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa