Ndipo akufulumiza anthu ndi akapitao ao anatuluka, nanena ndi anthu ndi kuti, Atero Farao, Kulibe kukupatsani udzu.
Eksodo 5:11 - Buku Lopatulika Mukani inu nokha, dzifunireni udzu komwe muupeza; pakuti palibe kanthu kadzachepa pa ntchito yanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mukani inu nokha, dzifunireni udzu komwe muupeza; pakuti palibe kanthu kadzachepa pa ntchito yanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Muzidzimwetera nokha kulikonse komwe mungaupeze. Koma chiŵerengero cha njerwa ndi chonchija.’ ” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mʼmalo mwake mupite mukadzimwetere udzu kulikonse kumene mungawupeze. Komabe ntchito yanu sichepetsedwa.’ ” |
Ndipo akufulumiza anthu ndi akapitao ao anatuluka, nanena ndi anthu ndi kuti, Atero Farao, Kulibe kukupatsani udzu.