Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




Eksodo 38:22 - Buku Lopatulika

Ndipo Bezalele mwana wa Uri, mwana wa Huri, wa fuko la Yuda, anapanga zonse zimene Yehova adauza Mose.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Ndipo Bezalele mwana wa Uri, mwana wa Huri, wa fuko la Yuda, anapanga zonse zimene Yehova adauza Mose.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Ndipo Bezalele, mwana wa Uri, mdzukulu wa Huri, wa fuko la Yuda, adapanga zonse zimene Chauta adalamula Mose kuti apange.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Bezaleli mwana wa Uri, mwana wa Huzi wa fuko la Yuda anapanga chilichonse Yehova analamulira Mose,

Onani mutuwo



Eksodo 38:22
7 Mawu Ofanana  

Ndi Huri anabala Uri, ndi Uri anabala Bezalele.


Pamenepo sindidzachita manyazi, pakupenyerera malamulo anu onse.


Ndipo Mose anati kwa ana a Israele, Taonani, Yehova anaitana, ndi kumtchula dzina lake, Bezalele, mwana wa Uri, mwana wa Huri, wa fuko la Yuda;


Ichi ndi chiwerengo cha zinthu za chihema, chihema cha mboni, monga anaziwerenga, monga mwa mau a Mose, achite nazo Alevi; anaziwerenga Itamara, mwana wa Aroni wansembe.


Koma Yehova anati kwa ine, Usati, ndine mwana pakuti udzanka kwa yense amene ndidzakutumako iwe, nudzanena chonse chimene ndidzakuuza.


ndi kuwaphunzitsa, asunge zinthu zonse zimene ndinakulamulani inu; ndipo onani, Ine ndili pamodzi ndi inu masiku onse, kufikira chimaliziro cha nthawi ya pansi pano.