Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 35:30 - Buku Lopatulika

30 Ndipo Mose anati kwa ana a Israele, Taonani, Yehova anaitana, ndi kumtchula dzina lake, Bezalele, mwana wa Uri, mwana wa Huri, wa fuko la Yuda;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Ndipo Mose anati kwa ana a Israele, Taonani, Yehova anaitana, ndi kumtchula dzina lake, Bezalele, mwana wa Uri, mwana wa Huri, wa fuko la Yuda;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Pambuyo pake Mose adauza Aisraele kuti, “Chauta wasankhula Bezalele, mwana wa Uri, mdzukulu wa Huri, wa fuko la Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Kenaka Mose anati kwa Aisraeli, “Taonani, Yehova wasankha Bezaleli mwana wa Uri, mwana wa Huri, wa fuko la Yuda,

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 35:30
8 Mawu Ofanana  

ndipo anamdzaza ndi mzimu wa Mulungu, ndi luso, ndi nzeru, ndi chidziwitso, za m'ntchito zilizonse;


Pakuti Mulungu wake amlangiza bwino namphunzitsa.


Koma zonse izi achita Mzimu mmodzi yemweyo, nagawira yense pa yekha monga afuna.


Ndipo pali mphatso zosiyana, koma Mzimu yemweyo.


Monga mwa chisomo cha Mulungu chidapatsidwa kwa ine, ngati mwini mamangidwe waluso, ndinaika maziko, koma wina amangapo. Koma yense ayang'anire umo amangira pamenepo.


Mphatso iliyonse yabwino, ndi chininkho chilichonse changwiro zichokera Kumwamba, zotsika kwa Atate wa mauniko, amene alibe chisanduliko, kapena mthunzi wa chitembenukiro.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa