Ndipo anapanga gome la mtengo wakasiya; utali wake mikono iwiri, ndi kupingasa kwake mkono umodzi, ndi msinkhu wake mkono ndi hafu;
Eksodo 37:11 - Buku Lopatulika ndipo analikuta ndi golide woona, nalipangira mkombero wagolide pozungulira pake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndipo analikuta ndi golide woona, nalipangira mkombero wagolide pozungulira pake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono adalikuta ndi golide wabwino kwambiri, nalemba mkombelo wagolide kuzungulira tebulo lonselo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka analikuta ndi golide wabwino kwambiri, ndipo anapanga mkombero wagolide mʼmbali mwake. |
Ndipo anapanga gome la mtengo wakasiya; utali wake mikono iwiri, ndi kupingasa kwake mkono umodzi, ndi msinkhu wake mkono ndi hafu;
Analipangiranso mitanda pozungulirapo, yoyesa chikhato m'kupingasa kwake, ndi pamitanda pake pozungulira anapangirapo mkombero wagolide.