Eksodo 28:23 - Buku Lopatulika Nupangire pa chapachifuwa mphete ziwiri zagolide, ndi kuzika mphete ziwirizo pansonga zake ziwiri za chapachifuwa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nupangire pa chapachifuwa mphete ziwiri zagolide, ndi kuzika mphete ziwirizo pa nsonga zake ziwiri za chapachifuwa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Upangenso mphete ziŵiri, ndipo uzilumikize pa ngodya zam'mwamba za chovala chapachifuwa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Upangenso mphete ziwiri zagolide ndipo uzimangirire pa ngodya ziwiri za pa chovala chapachifuwa. |