Eksodo 26:16 - Buku Lopatulika Utali wake wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwake kwa thabwali mkono ndi hafu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Utali wake wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwake kwa thabwali mkono ndi hafu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Muutali mwake fulemu lililonse likhale mamita anai ndi theka, ndipo muufupi mwake masentimita 69. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Feremu iliyonse ikhale yotalika mamita anayi ndipo mulifupi mwake mukhale masentimita 69. |
Pa thabwa limodzi pakhale mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; uzitero pa matabwa onse a chihema.