Munthu akakantha mnyamata wake, kapena mdzakazi wake, ndi ndodo, ndipo akafa padzanja pake; ameneyo alangidwe ndithu.
Eksodo 21:21 - Buku Lopatulika Koma akakhala wosafa tsiku limodzi kapena awiri, asalangike, pakuti ndiye ndalama ya mbuye wake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma akakhala wosafa tsiku limodzi kapena awiri, asalirike, pakuti ndiye ndalama ya mbuye wake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma kapoloyo akakhala moyo tsiku lathunthu kapena masiku aŵiri, mbuyakeyo asalangidwe. Kapoloyo ndi chuma cha mbuyakeyo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma ngati kapolo uja akhala ndi moyo tsiku lonse kapena masiku awiri, ndiye kuti mbuye uja asalangidwe chifukwa kapolo ndi chuma chake. |
Munthu akakantha mnyamata wake, kapena mdzakazi wake, ndi ndodo, ndipo akafa padzanja pake; ameneyo alangidwe ndithu.