Akamtengera mkazi wina, asachepetse chakudya chake, zovala zake, ndi za ukwati zakezake.
Eksodo 21:11 - Buku Lopatulika Ndipo akapanda kumchitira izi zitatu, azituluka chabe, osaperekapo ndalama. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo akapanda kumchitira izi zitatu, azituluka chabe, osaperekapo ndalama. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Akapanda kumchitira zimenezi, ammasule kuti akhale mfulu, koma osalandirapo ndalama. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma ngati sangathe kumuchitira zonsezi, ndiye amuleke apite popanda kulipira kanthu. |
Akamtengera mkazi wina, asachepetse chakudya chake, zovala zake, ndi za ukwati zakezake.