Ndipo ana a Israele anayenda ulendo wakuchokera ku Ramsesi kufikira ku Sukoti, zikwi mazana asanu ndi limodzi oyenda okha, ndiwo amuna, osawerenga ana.
Eksodo 13:20 - Buku Lopatulika Ndipo anachokera ku Sukoti, nagona ku Etamu, pa malekezero a chipululu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anachokera ku Sukoti, nagona ku Etamu, pa malekezero a chipululu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Aisraele adachoka ku Sukoti, nakagona ku Etamu m'mbali mwa chipululu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atachoka ku Sukoti anakagona ku Etamu mʼmphepete mwa chipululu. |
Ndipo ana a Israele anayenda ulendo wakuchokera ku Ramsesi kufikira ku Sukoti, zikwi mazana asanu ndi limodzi oyenda okha, ndiwo amuna, osawerenga ana.