Ndipo panali pamene Israele anakhala m'dzikomo, Rubeni anamuka nagona ndi Biliha, mkazi wamng'ono wa atate wake: ndipo Israele anamva. Ana aamuna a Yakobo anali khumi ndi awiri:
Eksodo 1:4 - Buku Lopatulika Dani ndi Nafutali, Gadi ndi Asere. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Dani ndi Nafutali, Gadi ndi Asere. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Dani, Nafutali, Gadi ndi Asere. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Dani, Nafutali; Gadi ndi Aseri. |
Ndipo panali pamene Israele anakhala m'dzikomo, Rubeni anamuka nagona ndi Biliha, mkazi wamng'ono wa atate wake: ndipo Israele anamva. Ana aamuna a Yakobo anali khumi ndi awiri:
Amenewa ndi ana a Zilipa, amene Labani anampatsa Leya mwana wake wamkazi, amenewo anambalira Yakobo, anthu khumi ndi asanu ndi mmodzi.
Ndipo amoyo onse amene anatuluka m'chuuno mwake mwa Yakobo ndiwo makumi asanu ndi awiri; koma Yosefe anali mu Ejipito.