Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 46:18 - Buku Lopatulika

18 Amenewa ndi ana a Zilipa, amene Labani anampatsa Leya mwana wake wamkazi, amenewo anambalira Yakobo, anthu khumi ndi asanu ndi mmodzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Amenewa ndi ana a Zilipa, amene Labani anampatsa Leya mwana wake wamkazi, amenewo anambalira Yakobo, anthu khumi ndi asanu ndi mmodzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 (Onseŵa anali adzukulu a Yakobe obadwa mwa Zilipa amene Labani adaapereka kwa mwana wake Leya.)

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Amenewa ndi zidzukulu za Yakobo mwa Zilipa amene Labani anapereka kwa mwana wake, Leya. Onse pamodzi analipo 16.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 46:18
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Labani anampatsa mwana wake wamkazi Leya Zilipa mdzakazi wake kuti akhale mdzakazi wa Leya.


ndipo ana aamuna a Zilipa mdzakazi wake wa Leya: ndiwo Gadi ndi Asere: amenewo ndi ana aamuna a Yakobo amene anabala iye mu Padanaramu.


Ndi ana aamuna a Asere: Imina, ndi Isiva, ndi Isivi, ndi Beriya, ndi Sera mlongo wao; ndi ana a Beriya: Hebere, ndi Malikiele.


Ana a Rakele mkazi wake wa Yakobo: Yosefe ndi Benjamini.


Dani ndi Nafutali, Gadi ndi Asere.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa