ana aamuna a Leya: ndiwo Rubeni mwana woyamba wa Yakobo, ndi Simeoni ndi Levi, ndi Yuda, ndi Zebuloni, ndi Isakara;
Eksodo 1:3 - Buku Lopatulika Isakara, Zebuloni, ndi Benjamini; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Isakara, Zebuloni, ndi Benjamini; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Isakara, Zebuloni, Benjamini, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Isakara, Zebuloni, Benjamini; |
ana aamuna a Leya: ndiwo Rubeni mwana woyamba wa Yakobo, ndi Simeoni ndi Levi, ndi Yuda, ndi Zebuloni, ndi Isakara;
ndi mzere wachinai wa tarisisi, sohamu, ndi yasefe; zikhale zogwirika ndi golide m'zoikamo zao.