Ndipo Mulungu wa mtendere adzaphwanya Satana pansi pa mapazi anu tsopano lino. Chisomo cha Ambuye wathu Yesu Khristu chikhale ndi inu nonse.
Afilipi 4:23 - Buku Lopatulika Chisomo cha Ambuye Yesu Khristu chikhale ndi mzimu wanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Chisomo cha Ambuye Yesu Khristu chikhale ndi mzimu wanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ambuye Yesu Khristu akudalitseni. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Chisomo cha Ambuye Yesu Khristu chikhale ndi mzimu wanu. Ameni. |
Ndipo Mulungu wa mtendere adzaphwanya Satana pansi pa mapazi anu tsopano lino. Chisomo cha Ambuye wathu Yesu Khristu chikhale ndi inu nonse.
Gayo, mwini nyumba wolandira ine, ndi Mpingo wonse wa Ambuye, akupereka moni. Erasto, ndiye woyang'anira mzinda, akupereka moni, ndiponso Kwarto mbaleyo.
Chisomo cha Ambuye Yesu Khristu, ndi chikondi cha Mulungu, ndi chiyanjano cha Mzimu Woyera zikhale ndi inu nonse.