Mwa ichi ndipempha kuti musade mtima m'zisautso zanga chifukwa cha inu, ndiwo ulemerero wanu.
Afilipi 2:18 - Buku Lopatulika momwemonso kondwerani inu, nimukondwere pamodzi ndi ine. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 momwemonso kondwerani inu, nimukondwere pamodzi ndi ine. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chimodzimodzi inunso muzikondwa, ndi kusangalala nane pamodzi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Chomwechonso, inu khalani okondwa ndi osangalala nane pamodzi. |
Mwa ichi ndipempha kuti musade mtima m'zisautso zanga chifukwa cha inu, ndiwo ulemerero wanu.
Komatu ngatinso ndithiridwa pa nsembe ndi kutumikira kwa chikhulupiriro chanu, ndikondwera, ndipo ndikondwera pamodzi ndi inu nonse;
Koma ndiyembekeza mwa Ambuye Yesu kuti ndidzatumiza Timoteo kwa inu msanga, kuti inenso nditonthozeke bwino pozindikira za kwa inu.
Chotsalira, abale anga, kondwerani mwa Ambuye. Kulembera zomwezo kwa inu, sikundivuta ine, koma kwa inu kuli kukhazikitsa.