Koma ndinena Ine choonadi ndi inu; kuyenera kwa inu kuti ndichoke Ine; pakuti ngati sindichoka, Nkhosweyo sadzadza kwa inu; koma ngati ndipita ndidzamtuma Iye kwa inu.
Afilipi 1:24 - Buku Lopatulika koma kukhalabe m'thupi ndiko kufunika koposa, chifukwa cha inu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 koma kukhalabe m'thupi ndiko kufunika koposa, chifukwa cha inu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma kwinakunso nkofunika kwambiri kuti ndikhale moyo chifukwa cha inuyo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Komanso nʼkofunika kwambiri kuti ndikhalebe mʼthupi chifukwa cha inu. |
Koma ndinena Ine choonadi ndi inu; kuyenera kwa inu kuti ndichoke Ine; pakuti ngati sindichoka, Nkhosweyo sadzadza kwa inu; koma ngati ndipita ndidzamtuma Iye kwa inu.
Koma ngati kukhala ndi moyo m'thupi ndiko chipatso cha ntchito yanga, sindizindikiranso chimene ndidzasankha.
Koma ndipanidwa nazo ziwirizi, pokhala nacho cholakalaka cha kuchoka kukhala ndi Khristu, ndiko kwabwino koposaposatu;