Wakhumi ndi chimodzi wa mwezi wakhumi ndi chimodzi ndiye Benaya Mpiratoni wa ana a Efuremu; ndi m'chigawo mwake zikwi makumi awiri mphambu zinai.
2 Samueli 23:30 - Buku Lopatulika Benaya Mpiratoni, Hidai wa ku timitsinje ta Gaasi; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Benaya Mpiratoni, Hidai wa ku timitsinje ta Gaasi; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Panalinso Benaya wa ku Piratoni, Hidai wa ku mitsinje ya ku Gaasi, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Benaya Mpiratoni, Hidayi wa ku zigwa za Gaasi. |
Wakhumi ndi chimodzi wa mwezi wakhumi ndi chimodzi ndiye Benaya Mpiratoni wa ana a Efuremu; ndi m'chigawo mwake zikwi makumi awiri mphambu zinai.
Ndipo anamuika m'malire a cholowa chake mu Timnati-Sera, ndiwo ku mapiri a Efuremu kumpoto kwa phiri la Gaasi.
Nafa Abidoni mwana wa Hilele wa ku Piratoni, naikidwa mu Piratoni m'dziko la Efuremu ku mapiri a Amaleke.
Ndipo anamuika m'malire a cholowa chake mu Timnati-Heresi, ku mapiri a Efuremu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.