Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Oweruza 2:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo anamuika m'malire a cholowa chake mu Timnati-Heresi, ku mapiri a Efuremu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo anamuika m'malire a cholowa chake m'Timnati-Heresi, ku mapiri a Efuremu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Ndipo adamuika m'dziko lake limene adalandira ngati choloŵa chake ku Timnati-Heresi m'dziko lamapiri la Efuremu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Ndipo anamuyika mʼmanda a mʼdziko lake, ku Timnati-Heresi mʼdziko la mapiri la Efereimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.

Onani mutuwo Koperani




Oweruza 2:9
6 Mawu Ofanana  

Ndipo atatha kuligawa dziko likhale cholowa chao monga mwa malire ake, ana a Israele anapatsa Yoswa mwana wa Nuni cholowa pakati pao;


monga mwa lamulo la Yehova anampatsa mzinda umene anawapempha, ndiwo Timnati-Sera, ku mapiri a Efuremu; ndipo anamanga mzindawo nakhala m'mwemo.


Ndipo kunali, zitatha izi, Yoswa mwana wa Nuni mtumiki wa Yehova, adafa, wa zaka zana ndi khumi.


Ndipo anamuika m'malire a cholowa chake mu Timnati-Sera, ndiwo ku mapiri a Efuremu kumpoto kwa phiri la Gaasi.


Ndipo atafa Yoswa, ana a Israele anafunsira kwa Yehova ndi kuti, Adzayamba ndani kutikwerera pa Akanani kuwathira nkhondo?


Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Yehova anafa wa zaka zake zana ndi khumi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa