Kazembe wachisanu wa mwezi wachisanu ndiye Samuti Mwizara; ndi m'chigawo mwake zikwi makumi awiri mphambu zinai.
2 Samueli 23:25 - Buku Lopatulika Sama Mharodi, Elika Mharodi; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Sama Mharodi, Elika Mharodi; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Sama wa ku Harodi, Elika wa ku Harodi Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Sama Mharodi, Elika Mherodi, |
Kazembe wachisanu wa mwezi wachisanu ndiye Samuti Mwizara; ndi m'chigawo mwake zikwi makumi awiri mphambu zinai.
Pamenepo Yerubaala, ndiye Gideoni, ndi anthu onse okhala naye anauka mamawa, namanga misasa pa chitsime cha Harodi, ndi misasa ya Midiyani inali kumpoto kwao, paphiri la More m'chigwa.