Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




2 Samueli 17:5 - Buku Lopatulika

Pomwepo Abisalomu anati, Kaitane tsopano Husai Mwariki yemwe, timvenso chimene anene iye.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Pomwepo Abisalomu anati, Kaitane tsopano Husai Mwariki yemwe, timvenso chimene anene iye.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Apo Abisalomu adati, “Muitanenso Husai, Mwariki, ndipo timvenso zimene anene.”

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Koma Abisalomu anati, “Muyitanenso Husai Mwariki kuti timve zimene iye adzanena.”

Onani mutuwo



2 Samueli 17:5
6 Mawu Ofanana  

Ndipo wina anauza Davide nati, Ahitofele ali pakati pa opangana chiwembu pamodzi ndi Abisalomu. Davide nati, Yehova, musandulize uphungu wa Ahitofele ukhale wopusa.


Ndipo mauwa anamuyenerera Abisalomu, ndi akulu onse a Israele.


Ndipo pakufika Husai kwa Abisalomu, Abisalomuyo ananena naye, Ahitofele analankhula mau akuti; tichite kodi monga mwa kunena kwake? Ngati iai, unene ndiwe.


nati kwa iwo, Kodi inu mundipangire bwanji kuti tiyankhe anthu awa anandiuza ine, kuti, Mupepuze goli limene atate wanu anatisenza ife?