Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




2 Samueli 11:22 - Buku Lopatulika

Chomwecho mthengawo unamuka, nufika, nudziwitsa Davide zonse Yowabu anamtumiza.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Chomwecho mthengawo unamuka, nufika, nudziwitsa Davide zonse Yowabu anamtumiza.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Wamthenga uja adapita, nakafika kwa Davide, nakamuuza zonse zimene Yowabu adamuuza kuti akanene.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Mthengayo ananyamuka, ndipo atafika anamuwuza Davide zonse zimene Yowabu anamutuma kuti akanene.

Onani mutuwo



2 Samueli 11:22
2 Mawu Ofanana  

Ndani anakantha Abimeleki mwana wa Yerubeseti? Sadamponyera kodi mphero mkazi wa palinga nafa iye ku Tebezi? Munasendera bwanji pafupi potere pa lingalo? Tsono udzanena, Mnyamata wanu Uriya Muhiti, iyenso adafa.


Ndipo mthengawo unati kwa Davide, Anthuwo anatipambana natulukira kwa ife kumundako, koma tinawagwera kufikira polowera kuchipata.