2 Samueli 11:19 - Buku Lopatulika nauza mthengawo kuti, Utatsiriza kuuza mfumu zonse za nkhondozo; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 nauza mthengawo kuti, Utatsiriza kuuza mfumu zonse za nkhondozo; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adauza wamthengayo kuti, “Utatha kumuuza mfumu mbiri yonse ya nkhondo, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iye anamulangiza wa mthengayo kuti, “Pamene ukatsiriza kufotokozera mfumu za ku nkhondozi, |
kudzali kuti ukapsa mtima wa mfumu nikati kwa iwe, Chifukwa ninji munayandikira pafupi potere pamzinda kukamenyana nao? Simunadziwe kodi kuti apalingawo adzaponya?