Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




1 Samueli 3:5 - Buku Lopatulika

Ndipo anathamangira kwa Eli nati, Ndine, popeza mwandiitana ine. Ndipo iye anati, Sindinaitane, kagone. Napita iye, nagona.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Ndipo anathamangira kwa Eli nati, Ndine, popeza mwandiitana ine. Ndipo iye anati, Sindinaitana, kagone. Napita iye, nagona.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Adathamangira kwa Eli nati, “Ndabwera, ndamva kuitana.” Koma Eli adati, “Sindidakuitane, kagone.” Motero Samuele adapita kukagona.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Ndipo iyeyo anathamangira kwa Eli ndipo anati, “Ndabwera ndamva kuyitana.” Koma Eli anati, “Ine sindinakuyitane, bwerera kagone.” Ndipo iye anapita kukagona.

Onani mutuwo



1 Samueli 3:5
2 Mawu Ofanana  

Pamenepo Yehova anaitana Samuele; ndipo iye anayankha kuti, Ndili pano.


Ndipo Yehova anabwereza kumuitana, ndi kuti, Samuele. Ndipo Samuele anauka, napita kwa Eli, nati, Ndine, pakuti mwandiitana ndithu. Koma iye anayankha, Sindinaitane, mwana wanga; kagone.