Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Samueli 3:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ndipo iyeyo anathamangira kwa Eli ndipo anati, “Ndabwera ndamva kuyitana.” Koma Eli anati, “Ine sindinakuyitane, bwerera kagone.” Ndipo iye anapita kukagona.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

5 Ndipo anathamangira kwa Eli nati, Ndine, popeza mwandiitana ine. Ndipo iye anati, Sindinaitane, kagone. Napita iye, nagona.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo anathamangira kwa Eli nati, Ndine, popeza mwandiitana ine. Ndipo iye anati, Sindinaitana, kagone. Napita iye, nagona.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Adathamangira kwa Eli nati, “Ndabwera, ndamva kuitana.” Koma Eli adati, “Sindidakuitane, kagone.” Motero Samuele adapita kukagona.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 3:5
2 Mawu Ofanana  

Yehova anayitana Samueli. Iye anayankha kuti, “Wawa.”


Yehova anayitananso, “Samueli!” Ndipo Samueli anadzuka ndi kupita kwa Eli nati, “Ndabwera popeza ndamva mukundiyitana.” Eli nati, “Mwana wanga, ine sindinakuyitane, bwerera kagone.”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa