Koma Davide akamuka kwa Saulo, nabwerera kudzadyetsa nkhosa za atate wake ku Betelehemu.
1 Samueli 18:2 - Buku Lopatulika Ndipo Saulo anamtenga tsiku lomwelo, osamlolanso apite kwao kwa atate wake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Saulo anamtenga tsiku lomwelo, osamlolanso apite kwao kwa atate wake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mwakuti adamtenga Davideyo tsiku lomwelo, osamlola kuti abwerere ku banja kwa bambo wake. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Choncho Sauli anamusunga Davideyo kuyambira tsiku limenelo ndipo sanamulole kuti abwerere ku nyumba ya abambo ake. |
Koma Davide akamuka kwa Saulo, nabwerera kudzadyetsa nkhosa za atate wake ku Betelehemu.
Pamenepo Yonatani anaitana Davide, namuuza zonsezi. Ndipo Yonatani anafika naye Davide kwa Saulo, iye nakhalanso pamaso pake monga kale.