1 Samueli 17:30 - Buku Lopatulika Napotolokera iye kwa munthu wina, nalankhula mau omwewo; ndipo anthu anamyankhanso monga momwemo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Napotolokera iye kwa munthu wina, nalankhula mau omwewo; ndipo anthu anamyankhanso monga momwemo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono adachoka apo napita kwa wina namufunsa zokhazokhazo. Aliyense adamuyankhanso monga poyamba paja. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo anamuchokera napita kwa munthu wina ndipo anamufunsa nkhani yomweyo, ndipo anthu anamuyankha iye monga poyamba paja. |
Ndipo pamene mau adanena Davide anamveka, anawapitiriza kwa Saulo; ndipo iye anamuitana.