Eksodo 2:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Iye anayankha kuti, “Inde, pita.” Ndipo mtsikanayo anapita nakayitana amayi a mwanayo. Onani mutuwoBuku Lopatulika8 Ndipo mwana wamkazi wa Farao ananena naye, Pita. Napita namwaliyo, nakaitana amake wa mwanayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo mwana wamkazi wa Farao ananena naye, Pita. Napita namwaliyo, nakaitana amake wa mwanayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 “Chabwino, pita.” Mlongo wakeyo adapita nakaitana amai ake a mwanayo. Onani mutuwo |